Yeremiya 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu awa uwauze kuti,‘Maso anga atulutse misozi usiku ndi masana ndipo asasiye,+Chifukwa mwana wamkazi wa anthu anga, yemwe ndi namwali, waphwanyidwa kotheratu+Ndipo ali ndi bala lalikulu kwambiri. Danieli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu mwachitadi zimene munachenjeza kuti mudzachitira ifeyo+ ndi atsogoleri athu amene ankatilamulira.* Mwachita zimenezi potigwetsera tsoka lalikulu. Zimene zachitika mu Yerusalemu sizinayambe zachitikapo padziko lonse lapansi.+
17 Anthu awa uwauze kuti,‘Maso anga atulutse misozi usiku ndi masana ndipo asasiye,+Chifukwa mwana wamkazi wa anthu anga, yemwe ndi namwali, waphwanyidwa kotheratu+Ndipo ali ndi bala lalikulu kwambiri.
12 Inu mwachitadi zimene munachenjeza kuti mudzachitira ifeyo+ ndi atsogoleri athu amene ankatilamulira.* Mwachita zimenezi potigwetsera tsoka lalikulu. Zimene zachitika mu Yerusalemu sizinayambe zachitikapo padziko lonse lapansi.+