Ezekieli 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzachita nawo pangano lamtendere+ ndipo pangano limeneli lidzakhalapo mpaka kalekale. Ine ndidzachititsa kuti akhazikike mʼdzikolo ndipo ndidzawachulukitsa+ komanso ndidzaika malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.
26 Ndidzachita nawo pangano lamtendere+ ndipo pangano limeneli lidzakhalapo mpaka kalekale. Ine ndidzachititsa kuti akhazikike mʼdzikolo ndipo ndidzawachulukitsa+ komanso ndidzaika malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.