Obadiya 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mtima wako wodzikuza wakupusitsa,+Iwe amene ukukhala mʼmalo obisika amʼthanthwe,Uli pamwamba pa phiri nʼkumanena mumtima mwako kuti,‘Ndani angandigwetsere pansi?’
3 Mtima wako wodzikuza wakupusitsa,+Iwe amene ukukhala mʼmalo obisika amʼthanthwe,Uli pamwamba pa phiri nʼkumanena mumtima mwako kuti,‘Ndani angandigwetsere pansi?’