Salimo 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo sinthani mmene ndimaganizira+ kuti ndikhale wokhulupirika. Ezekieli 11:19, 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala mʼmatupi awo+ nʼkuwapatsa mtima wamnofu,*+ 20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga komanso kumvera zigamulo zanga. Akadzatero adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’
10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo sinthani mmene ndimaganizira+ kuti ndikhale wokhulupirika.
19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala mʼmatupi awo+ nʼkuwapatsa mtima wamnofu,*+ 20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga komanso kumvera zigamulo zanga. Akadzatero adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’