-
Ezekieli 36:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 ‘Ndidzayeretsadi dzina langa lalikulu+ limene linadetsedwa pakati pa anthu a mitundu ina. Inu munadetsa dzina langalo pakati pa anthu a mitundu ina. Anthu a mitundu inawo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,+ akadzaona zimene ndakuchitirani komanso adzadziwa kuti ndine Mulungu woyera,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
-