Yesaya 60:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo, udzaona zimenezi ndipo nkhope yako idzasangalala.+Mtima wako udzagunda mwamphamvu ndipo udzasangalala kwambiri,Chifukwa chuma chamʼnyanja adzachibweretsa kwa iwe.Katundu wa mitundu ya anthu adzabwera kwa iwe.+ Yesaya 61:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzatchedwa ansembe a Yehova.+Anthu adzakutchulani kuti atumiki a Mulungu wathu. Mudzadya zinthu zochokera kumitundu ya anthu+Ndiponso mudzadzitamandira chifukwa cha ulemerero umene* mudzapeze kuchokera kwa iwo.
5 Pa nthawi imeneyo, udzaona zimenezi ndipo nkhope yako idzasangalala.+Mtima wako udzagunda mwamphamvu ndipo udzasangalala kwambiri,Chifukwa chuma chamʼnyanja adzachibweretsa kwa iwe.Katundu wa mitundu ya anthu adzabwera kwa iwe.+
6 Inuyo mudzatchedwa ansembe a Yehova.+Anthu adzakutchulani kuti atumiki a Mulungu wathu. Mudzadya zinthu zochokera kumitundu ya anthu+Ndiponso mudzadzitamandira chifukwa cha ulemerero umene* mudzapeze kuchokera kwa iwo.