15 Anthu onse odutsa mumsewu akakuona, akuwomba mʼmanja monyoza.+
Akuimba mluzu modabwa+ ndipo akupukusira mitu yawo mwana wamkazi wa Yerusalemu. Iwo akunena kuti:
“Kodi uwu ndi mzinda umene ankaunena kuti, ‘Ndi wokongola kwambiri ndipo anthu padziko lonse lapansi amasangalala nawoʼ?”+