Yeremiya 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndikapita kunja kwa mzinda,Ndikuona anthu ophedwa ndi lupanga.+ Ndipo ndikalowa mumzinda,+Ndikuona matenda obwera chifukwa cha njala. Aneneri komanso ansembe, onse apita kudziko lachilendo limene sakulidziwa.’”+
18 Ndikapita kunja kwa mzinda,Ndikuona anthu ophedwa ndi lupanga.+ Ndipo ndikalowa mumzinda,+Ndikuona matenda obwera chifukwa cha njala. Aneneri komanso ansembe, onse apita kudziko lachilendo limene sakulidziwa.’”+