-
Ezekieli 42:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti: “Nyumba zodyera zakumpoto ndi zakumʼmwera zimene zili pafupi ndi malo opanda kanthu,+ ndi nyumba zodyera zopatulika, kumene ansembe otumikira Yehova amadyerako nsembe zopatulika koposa.+ Mʼnyumbazo amaikamo nsembe zopatulika koposa zomwe ndi nsembe zambewu, nsembe zamachimo ndi nsembe zakupalamula, chifukwa malo amenewa ndi oyera.+
-