Deuteronomo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzipita kwa Alevi omwe ndi ansembe ndi kwa woweruza+ amene akutumikira mʼmasiku amenewo. Muziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuzani chigamulo.+
9 Muzipita kwa Alevi omwe ndi ansembe ndi kwa woweruza+ amene akutumikira mʼmasiku amenewo. Muziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuzani chigamulo.+