3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita mʼtsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense mmodzi ndi mmodzi ndipo onse anakwana 38,000. 4 Pa anthu amenewa, 24,000 anali oyangʼanira ntchito yapanyumba ya Yehova. Akapitawo ndi oweruza analipo 6,000.+