-
Yoswa 21:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Tsopano atsogoleri a mabanja a Alevi, anapita kwa wansembe Eliezara,+ Yoswa mwana wa Nuni ndi kwa atsogoleri a mafuko a Isiraeli. 2 Analankhula nawo ku Silo+ mʼdziko la Kanani, kuti: “Kudzera mwa Mose, Yehova analamula kuti tipatsidwe mizinda yoti tizikhalamo komanso malo oti tizidyetserako ziweto zathu.”+
-