Ezekieli 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Khomo lolowera linali mikono 10 mulifupi, ndipo makoma apakhomopo anali* mikono 5 mbali imodzi, ndi mikono 5 mbali inayo. Anayeza chipinda chakunja ndipo anapeza kuti chinali mikono 40 mulitali, mulifupi chinali mikono 20.
2 Khomo lolowera linali mikono 10 mulifupi, ndipo makoma apakhomopo anali* mikono 5 mbali imodzi, ndi mikono 5 mbali inayo. Anayeza chipinda chakunja ndipo anapeza kuti chinali mikono 40 mulitali, mulifupi chinali mikono 20.