Zekariya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa tsikulo madzi amoyo+ adzatuluka mu Yerusalemu.+ Hafu ya madziwo idzapita kunyanja yakumʼmawa*+ ndipo hafu inayo idzapita kunyanja ya kumadzulo.*+ Zimenezi zidzachitika mʼnyengo yotentha ndiponso mʼnyengo yozizira.
8 Pa tsikulo madzi amoyo+ adzatuluka mu Yerusalemu.+ Hafu ya madziwo idzapita kunyanja yakumʼmawa*+ ndipo hafu inayo idzapita kunyanja ya kumadzulo.*+ Zimenezi zidzachitika mʼnyengo yotentha ndiponso mʼnyengo yozizira.