11 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Pali ine Mulungu wamoyo, chifukwa chakuti iwe unaipitsa malo anga opatulika ndi mafano ako onse onyansa komanso zinthu zonse zonyansa zimene unkachita,+ inenso ndidzakukana. Diso langa silidzakumvera chisoni ndipo sindidzakuchitira chifundo.+