19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala mʼmatupi awo+ nʼkuwapatsa mtima wamnofu,+ 20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga komanso kumvera zigamulo zanga. Akadzatero adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’