Yesaya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+Anthu olemedwa ndi zolakwa,Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa. Iwo asiya Yehova.+Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.Iwo atembenuka nʼkumusiya. Yeremiya 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo inu mwachita zinthu zoipa kwambiri kuposa makolo anu.+ Aliyense wa inu akupitiriza kuumitsa khosi nʼkumatsatira mtima wake woipawo mʼmalo mondimvera.+
4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+Anthu olemedwa ndi zolakwa,Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa. Iwo asiya Yehova.+Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.Iwo atembenuka nʼkumusiya.
12 Ndipo inu mwachita zinthu zoipa kwambiri kuposa makolo anu.+ Aliyense wa inu akupitiriza kuumitsa khosi nʼkumatsatira mtima wake woipawo mʼmalo mondimvera.+