Genesis 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Yuda anapatuka nʼkupita pamene panali mkaziyo mʼmbali mwa msewu nʼkumuuza kuti: “Ndikufuna ndigone nawe.” Anamuuza zimenezi chifukwa sankadziwa kuti anali mpongozi wake.+ Koma mkaziyo anayankha kuti: “Mundipatsa chiyani kuti mugone nane?”
16 Choncho Yuda anapatuka nʼkupita pamene panali mkaziyo mʼmbali mwa msewu nʼkumuuza kuti: “Ndikufuna ndigone nawe.” Anamuuza zimenezi chifukwa sankadziwa kuti anali mpongozi wake.+ Koma mkaziyo anayankha kuti: “Mundipatsa chiyani kuti mugone nane?”