2 Mbiri 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zedekiya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 21 ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ 2 Mbiri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anagalukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inamulumbiritsa mʼdzina la Mulungu. Zedekiya anapitiriza kukhala wosamva komanso kuumitsa mtima wake ndipo anakana kubwerera kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.
13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anagalukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inamulumbiritsa mʼdzina la Mulungu. Zedekiya anapitiriza kukhala wosamva komanso kuumitsa mtima wake ndipo anakana kubwerera kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.