17 Ndiyeno Yeremiya anauza Zedekiya kuti: “Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Mukadzipereka mʼmanja mwa akalonga a mfumu ya Babulo, mudzakhalabe ndi moyo ndipo mzindawu sudzawotchedwa ndi moto komanso inuyo ndi banja lanu mudzakhalabe ndi moyo.+