-
Yeremiya 31:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 “Ndamva Efuraimu akulira kuti,
‘Ndinali ngati mwana wa ngʼombe wosaphunzitsidwa,
Mwandidzudzula ndipo ndaphunzirapo kanthu.
Ndithandizeni kuti ndibwerere ndipo ndidzabwereradi,
Chifukwa inu ndinu Yehova Mulungu wanga.
-