-
Ezekieli 21:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno akakufunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani ukubuula?’ Uwayankhe kuti, ‘Nʼchifukwa cha uthenga umene ndamva.’ Chifukwa zimene ndamvazo zidzachitikadi ndipo mtima wa munthu aliyense udzasungunuka ndi mantha. Manja a anthu onse adzafooka. Aliyense adzataya mtima ndipo mawondo onse azidzangochucha madzi.*+ ‘Uthengawo ufika ndithu ndipo zimene ukunena zidzachitikadi,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
-