Ezekieli 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 kapena akamayenda, mawilo aja ankayenda nawo limodzi ali pambali pawo. Akerubiwo akakweza mapiko awo kuti akwere mʼmwamba, mawilowo sankatembenuka kapena kuchoka pambali pawo.+
16 kapena akamayenda, mawilo aja ankayenda nawo limodzi ali pambali pawo. Akerubiwo akakweza mapiko awo kuti akwere mʼmwamba, mawilowo sankatembenuka kapena kuchoka pambali pawo.+