Deuteronomo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo anthu ochepa okha pakati panu ndi amene adzapulumuke+ mʼmayiko a mitundu imene Yehova adzakuthamangitsireni. Deuteronomo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzachititsa kuti adani anu akugonjetseni.+ Popita kukawaukira mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa mudzadutsa njira zosiyanasiyana 7. Mafumu onse a dziko lapansi adzachita mantha akadzaona zinthu zoipa zimene zakuchitikirani.+
27 Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo anthu ochepa okha pakati panu ndi amene adzapulumuke+ mʼmayiko a mitundu imene Yehova adzakuthamangitsireni.
25 Yehova adzachititsa kuti adani anu akugonjetseni.+ Popita kukawaukira mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa mudzadutsa njira zosiyanasiyana 7. Mafumu onse a dziko lapansi adzachita mantha akadzaona zinthu zoipa zimene zakuchitikirani.+