Levitiko 11:46, 47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Limeneli ndi lamulo lokhudza nyama, zamoyo zouluka, zamoyo zonse zamʼmadzi ndi zamoyo zonse zapamtunda, 47 kuti muzisiyanitsa chodetsedwa ndi choyera komanso zamoyo zimene muyenera kudya ndi zimene simukuyenera kudya.’”+
46 Limeneli ndi lamulo lokhudza nyama, zamoyo zouluka, zamoyo zonse zamʼmadzi ndi zamoyo zonse zapamtunda, 47 kuti muzisiyanitsa chodetsedwa ndi choyera komanso zamoyo zimene muyenera kudya ndi zimene simukuyenera kudya.’”+