2 Nditayangʼana ndinaona chinachake chooneka ngati moto. Ndipo moto unkayaka kuchokera pachimene chinkaoneka ngati chiuno chake kupita mʼmunsi.+ Kuchokera mʼchiuno mwake kupita mʼmwamba, maonekedwe ake anali owala ngati siliva wosakanikirana ndi golide.+