Levitiko 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngati munthu wa Chiisiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu wapita kokasaka, ndipo wagwira nyama kapena mbalame imene munaloledwa kuti muzidya, azithira magazi ake pansi+ nʼkuwakwirira ndi dothi. Deuteronomo 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma musamadye magazi ake.+ Muziwathira pansi ngati madzi.+
13 Ngati munthu wa Chiisiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu wapita kokasaka, ndipo wagwira nyama kapena mbalame imene munaloledwa kuti muzidya, azithira magazi ake pansi+ nʼkuwakwirira ndi dothi.