Salimo 74:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anawotcha malo anu opatulika.+ Anaipitsa chihema chokhala ndi dzina lanu nʼkuchigwetsera pansi. Salimo 79:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa mʼdziko limene ndi cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Yerusalemu amusandutsa bwinja.+ Yeremiya 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho nyumba imene ikudziwika ndi dzina langa,+ imene mukuidalira+ ndiponso pamalo awa amene ndinawapereka kwa inu ndi makolo anu, ndidzachita zofanana ndi zimene ndinachita ku Silo.+ Maliro 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani wamulanda zinthu zake zonse zamtengo wapatali.+ Yerusalemu waona anthu a mitundu ina akulowa mʼmalo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isamalowe mumpingo wanu. Maliro 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wakana guwa lake lansembe.Iye wasiya malo ake opatulika.+ Wapereka mʼmanja mwa adani makoma a nsanja zake zotetezeka.+ Adaniwo afuula mʼnyumba ya Yehova+ ngati pa tsiku lachikondwerero. Ezekieli 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anawauza kuti: “Ipitsani nyumbayi ndipo mudzaze mabwalo ake ndi mitembo ya anthu ophedwa.+ Pitani!” Choncho iwo anapitadi nʼkukapha anthu mumzindamo.
79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa mʼdziko limene ndi cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Yerusalemu amusandutsa bwinja.+
14 Choncho nyumba imene ikudziwika ndi dzina langa,+ imene mukuidalira+ ndiponso pamalo awa amene ndinawapereka kwa inu ndi makolo anu, ndidzachita zofanana ndi zimene ndinachita ku Silo.+
10 Mdani wamulanda zinthu zake zonse zamtengo wapatali.+ Yerusalemu waona anthu a mitundu ina akulowa mʼmalo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isamalowe mumpingo wanu.
7 Yehova wakana guwa lake lansembe.Iye wasiya malo ake opatulika.+ Wapereka mʼmanja mwa adani makoma a nsanja zake zotetezeka.+ Adaniwo afuula mʼnyumba ya Yehova+ ngati pa tsiku lachikondwerero.
7 Kenako anawauza kuti: “Ipitsani nyumbayi ndipo mudzaze mabwalo ake ndi mitembo ya anthu ophedwa.+ Pitani!” Choncho iwo anapitadi nʼkukapha anthu mumzindamo.