1 Mafumu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mʼzombomo, Hiramu ankatumizamo antchito ake odziwa bwino zapanyanja+ kuti akagwire ntchito limodzi ndi antchito a Solomo.
27 Mʼzombomo, Hiramu ankatumizamo antchito ake odziwa bwino zapanyanja+ kuti akagwire ntchito limodzi ndi antchito a Solomo.