2 Mafumu 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi milungu ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawapulumutsa? Kodi inapulumutsa Gozani, Harana,+ Rezefi ndi anthu a ku Edeni amene anali ku Tela-sara? Amosi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzathyola mipiringidzo ya mageti a Damasiko.+Ndidzapha anthu a ku Bikati-aveni,Komanso wolamulira* ku Beti-edeni.Ndipo anthu a ku Siriya adzapita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’
12 Kodi milungu ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawapulumutsa? Kodi inapulumutsa Gozani, Harana,+ Rezefi ndi anthu a ku Edeni amene anali ku Tela-sara?
5 Ndidzathyola mipiringidzo ya mageti a Damasiko.+Ndidzapha anthu a ku Bikati-aveni,Komanso wolamulira* ku Beti-edeni.Ndipo anthu a ku Siriya adzapita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’