Ezekieli 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakusandutsa thanthwe losalala lopanda kanthu ndipo udzakhala malo oyanikapo makoka.+ Mzinda wako sudzamangidwanso chifukwa ine Yehova ndanena,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
14 Ndidzakusandutsa thanthwe losalala lopanda kanthu ndipo udzakhala malo oyanikapo makoka.+ Mzinda wako sudzamangidwanso chifukwa ine Yehova ndanena,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.