-
Ezekieli 21:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Maula amene adzakhale mʼdzanja lake lamanja, adzasonyeza kuti apite ku Yerusalemu, akaike zida zogumulira mzindawo, akalamule asilikali ake kuti aphe anthu, akalize chizindikiro cha nkhondo, akaike zida zogumulira mageti a mzindawo, akamange malo okwera omenyerapo nkhondo ndiponso kuti akamange mpanda womenyerapo nkhondo.+
-