Yesaya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uwu ndi uthenga wokhudza Babulo,+ umene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona mʼmasomphenya: Yesaya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa nyenyezi zakumwamba ndi magulu awo*+Sizidzaonetsa kuwala kwawo.Dzuwa lidzachita mdima potuluka,Ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.
10 Chifukwa nyenyezi zakumwamba ndi magulu awo*+Sizidzaonetsa kuwala kwawo.Dzuwa lidzachita mdima potuluka,Ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.