Ezekieli 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzaumitsa ngalande zamumtsinje wa Nailo+ ndipo ndidzagulitsa dzikolo kwa anthu oipa. Ndidzachititsa kuti dzikolo ndi zonse zimene zili mmenemo ziwonongedwe ndi anthu ochokera kudziko lina.+ Ine Yehova, ndanena zimenezi.’
12 Ndidzaumitsa ngalande zamumtsinje wa Nailo+ ndipo ndidzagulitsa dzikolo kwa anthu oipa. Ndidzachititsa kuti dzikolo ndi zonse zimene zili mmenemo ziwonongedwe ndi anthu ochokera kudziko lina.+ Ine Yehova, ndanena zimenezi.’