Ezekieli 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ‘Kodi ine ndimasangalala ndi imfa ya munthu wochimwa?+ Kodi zimene ine ndimafuna si zoti munthu wochimwayo alape nʼkupitiriza kukhala ndi moyo?’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. 1 Timoteyo 2:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimenezi ndi zabwino ndiponso zovomerezeka kwa Mulungu, yemwe ndi Mpulumutsi wathu,+ 4 amene amafuna kuti anthu osiyanasiyana apulumuke+ nʼkukhala odziwa choonadi molondola.
23 ‘Kodi ine ndimasangalala ndi imfa ya munthu wochimwa?+ Kodi zimene ine ndimafuna si zoti munthu wochimwayo alape nʼkupitiriza kukhala ndi moyo?’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
3 Zimenezi ndi zabwino ndiponso zovomerezeka kwa Mulungu, yemwe ndi Mpulumutsi wathu,+ 4 amene amafuna kuti anthu osiyanasiyana apulumuke+ nʼkukhala odziwa choonadi molondola.