Ezekieli 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma inu mudzanena kuti: “Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.”+ Tamverani inu a nyumba ya Isiraeli. Kodi njira zanga nʼzimene zili zopanda chilungamo?+ Kodi njira zanu si zimene zili zopanda chilungamo?+ Ezekieli 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma nyumba ya Isiraeli idzanena kuti: “Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.” Kodi nʼzoona kuti njira zanga nʼzimene zili zopanda chilungamo, inu a nyumba ya Isiraeli?+ Kodi njira zanu si zimene zili zopanda chilungamo?’
25 Koma inu mudzanena kuti: “Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.”+ Tamverani inu a nyumba ya Isiraeli. Kodi njira zanga nʼzimene zili zopanda chilungamo?+ Kodi njira zanu si zimene zili zopanda chilungamo?+
29 Koma nyumba ya Isiraeli idzanena kuti: “Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.” Kodi nʼzoona kuti njira zanga nʼzimene zili zopanda chilungamo, inu a nyumba ya Isiraeli?+ Kodi njira zanu si zimene zili zopanda chilungamo?’