Deuteronomo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati: “Yehova anabwera kuchokera ku Sinai,+Anawala pa iwo kuchokera ku Seiri. Anawala mwa ulemerero kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi angelo ake ambirimbiri,*+Kudzanja lake lamanja kunali asilikali ake.+ 1 Mafumu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+ Salimo 68:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali mʼmagulu a masauzande osawerengeka, ali mʼmagulu masauzandemasauzande.+ Yehova walowa mʼmalo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+ Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,* Yuda 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhalenso Inoki,+ wa mʼbadwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova* anabwera ndi angelo ake masauzandemasauzande+ Chivumbulutso 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako, ndinaona ndi kumva mawu a angelo ambiri atazungulira mpando wachifumu limodzi ndi angelo 4 komanso akulu aja. Chiwerengero chawo chinali 10 sauzande kuchulukitsa ndi 10 sauzande* ndiponso mamiliyoni kuchulukitsa ndi masauzande.+
2 Iye anati: “Yehova anabwera kuchokera ku Sinai,+Anawala pa iwo kuchokera ku Seiri. Anawala mwa ulemerero kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi angelo ake ambirimbiri,*+Kudzanja lake lamanja kunali asilikali ake.+
19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+
17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali mʼmagulu a masauzande osawerengeka, ali mʼmagulu masauzandemasauzande.+ Yehova walowa mʼmalo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+
22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,*
14 Ngakhalenso Inoki,+ wa mʼbadwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova* anabwera ndi angelo ake masauzandemasauzande+
11 Kenako, ndinaona ndi kumva mawu a angelo ambiri atazungulira mpando wachifumu limodzi ndi angelo 4 komanso akulu aja. Chiwerengero chawo chinali 10 sauzande kuchulukitsa ndi 10 sauzande* ndiponso mamiliyoni kuchulukitsa ndi masauzande.+