Mateyu 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako chizindikiro cha Mwana wa munthu chidzaonekera kumwamba ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni.+ Iwo adzaona Mwana wa munthu+ akubwera pamitambo ya kumwamba ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+ Luka 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako adzaona Mwana wa munthu+ akubwera mumtambo ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+ Yohane 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipotu palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+ Machitidwe 7:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Ndipo ananena kuti: “Taonani! Ndikuona kumwamba kutatseguka, ndipo Mwana wa munthu+ waima kudzanja lamanja la Mulungu.”+ Chivumbulutso 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona mtambo woyera. Pamtambopo panali patakhala winawake wooneka ngati mwana wa munthu,+ atavala chisoti chachifumu chagolide kumutu kwake ndipo mʼdzanja lake munali chikwakwa chakuthwa.
30 Kenako chizindikiro cha Mwana wa munthu chidzaonekera kumwamba ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni.+ Iwo adzaona Mwana wa munthu+ akubwera pamitambo ya kumwamba ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+
13 Ndipotu palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+
56 Ndipo ananena kuti: “Taonani! Ndikuona kumwamba kutatseguka, ndipo Mwana wa munthu+ waima kudzanja lamanja la Mulungu.”+
14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona mtambo woyera. Pamtambopo panali patakhala winawake wooneka ngati mwana wa munthu,+ atavala chisoti chachifumu chagolide kumutu kwake ndipo mʼdzanja lake munali chikwakwa chakuthwa.