-
Danieli 2:39, 40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Koma pambuyo panu padzabwera ufumu+ wina wotsikirapo kwa inu. Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wakopa, umene udzalamulire dziko lonse lapansi.+
40 Ufumu wa nambala 4 udzakhala wolimba ngati chitsulo.+ Mofanana ndi chitsulo chimene chimaphwanya nʼkupera china chilichonse, ufumuwo udzaphwanya nʼkuwonongeratu maufumu ena onsewa.+
-