Danieli 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma pambuyo panu padzabwera ufumu+ wina wotsikirapo kwa inu. Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wakopa, umene udzalamulire dziko lonse lapansi.+ Danieli 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinapitiriza kuyangʼana ndipo ndinaona chilombo china chooneka ngati kambuku+ koma chinali ndi mapiko 4 pamsana pake ooneka ngati a mbalame. Chilombochi chinali ndi mitu 4+ ndipo chinapatsidwa ulamuliro. Danieli 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+
39 Koma pambuyo panu padzabwera ufumu+ wina wotsikirapo kwa inu. Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wakopa, umene udzalamulire dziko lonse lapansi.+
6 Kenako ndinapitiriza kuyangʼana ndipo ndinaona chilombo china chooneka ngati kambuku+ koma chinali ndi mapiko 4 pamsana pake ooneka ngati a mbalame. Chilombochi chinali ndi mitu 4+ ndipo chinapatsidwa ulamuliro.
21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+