17 Choncho iye anabwera pafupi ndi pamene ine ndinaima. Koma atafika, ndinachita mantha kwambiri ndipo ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi. Ndiyeno anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, dziwa kuti masomphenyawa ndi okhudza nthawi yamapeto.”+