Salimo 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu ndinu kasupe wa moyo.+Chifukwa cha kuwala kochokera kwa inu, timaona kuwala.+ Salimo 112:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kwa anthu owongoka mtima iye amawala ngati kuwala kumene kumaunika mumdima.+ ח [Heth] Iye ndi wokoma mtima,* wachifundo+ komanso wolungama.
4 Kwa anthu owongoka mtima iye amawala ngati kuwala kumene kumaunika mumdima.+ ח [Heth] Iye ndi wokoma mtima,* wachifundo+ komanso wolungama.