Chivumbulutso 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nditamuona, ndinagwera pamapazi ake ngati kuti ndafa. Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja nʼkundiuza kuti: “Usachite mantha. Ine ndine Woyamba+ ndi Womaliza,+
17 Nditamuona, ndinagwera pamapazi ake ngati kuti ndafa. Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja nʼkundiuza kuti: “Usachite mantha. Ine ndine Woyamba+ ndi Womaliza,+