Danieli 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mfumu inalamula Asipenazi, mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu kuti abweretse ena mwa Aisiraeli,* kuphatikizapo a mʼbanja lachifumu komanso anthu olemekezeka.+ Danieli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pagulu la anyamatawo panali anyamata ena a fuko la Yuda.* Mayina awo anali Danieli,*+ Hananiya,* Misayeli* ndi Azariya.*+
3 Ndiyeno mfumu inalamula Asipenazi, mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu kuti abweretse ena mwa Aisiraeli,* kuphatikizapo a mʼbanja lachifumu komanso anthu olemekezeka.+
6 Pagulu la anyamatawo panali anyamata ena a fuko la Yuda.* Mayina awo anali Danieli,*+ Hananiya,* Misayeli* ndi Azariya.*+