Genesis 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anamuyankha kuti: “Talota maloto, koma palibe woti atimasulire malotowo.” Yosefe anawauza kuti: “Kodi Mulungu si amene amamasulira?+ Ndifotokozereni malotowo.” Danieli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu woona anachititsa kuti anyamata* 4 amenewa akhale odziwa zinthu komanso ozindikira zinthu zonse zolembedwa ndipo anawapatsa nzeru. Danieli anamupatsa nzeru zoti azitha kumvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+
8 Iwo anamuyankha kuti: “Talota maloto, koma palibe woti atimasulire malotowo.” Yosefe anawauza kuti: “Kodi Mulungu si amene amamasulira?+ Ndifotokozereni malotowo.”
17 Mulungu woona anachititsa kuti anyamata* 4 amenewa akhale odziwa zinthu komanso ozindikira zinthu zonse zolembedwa ndipo anawapatsa nzeru. Danieli anamupatsa nzeru zoti azitha kumvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+