32 ndipo akuthamangitsa pakati pa anthu. Uzikhala ndi nyama zakutchire ndipo uzidya udzu ngati ngʼombe. Ndiyeno padutsa nthawi zokwana 7 mpaka utadziwa kuti Mulungu Wamʼmwambamwamba ndi Wolamulira wa maufumu a anthu, ndiponso kuti amapereka ulamuliro kwa aliyense amene akufuna kumupatsa.’”+