Deuteronomo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukadzalandira cholowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu musamadzasunthe zizindikiro za malire a mnzanu,+ pamalo amene makolo anu anaika kale malire.
14 Mukadzalandira cholowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu musamadzasunthe zizindikiro za malire a mnzanu,+ pamalo amene makolo anu anaika kale malire.