Hoseya 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo akafika mpaka kudziko la Asuri+ ngati bulu wamʼtchire. Efuraimu walipira akazi kuti azigona nawo.+ Hoseya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Efuraimu akudya mphepo. Akuthamangitsa mphepo yakumʼmawa tsiku lonse. Iye akuchulukitsa mabodza ndi chiwawa. Wachita pangano ndi Asuri+ ndipo wapititsa mafuta ku Iguputo.+
9 Iwo akafika mpaka kudziko la Asuri+ ngati bulu wamʼtchire. Efuraimu walipira akazi kuti azigona nawo.+
12 “Efuraimu akudya mphepo. Akuthamangitsa mphepo yakumʼmawa tsiku lonse. Iye akuchulukitsa mabodza ndi chiwawa. Wachita pangano ndi Asuri+ ndipo wapititsa mafuta ku Iguputo.+