Hoseya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli amira mʼzinthu zowononga ngati mʼmasiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo nʼkuwalanga chifukwa cha machimo awo.+ Amosi 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo,+ walumbira mogwirizana ndi dzina lake kuti:‘Sindidzaiwala zochita zawo zonse.+
9 Aisiraeli amira mʼzinthu zowononga ngati mʼmasiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo nʼkuwalanga chifukwa cha machimo awo.+
7 Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo,+ walumbira mogwirizana ndi dzina lake kuti:‘Sindidzaiwala zochita zawo zonse.+