25 Ndi zofanananso ndi zimene ananena mʼbuku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatchula kuti ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sankakondedwa ndidzamutchula kuti ‘wokondedwa.’+ 26 Kumene ankauzidwa kuti, ‘Siinu anthu anga,’ adzauzidwa kuti, ‘Ndinu ana a Mulungu wamoyo.’”+